-
Ezekieli 41:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Kenako anayeza kumaso kwa kachisi m’lifupi mwake limodzi ndi mpata waukulu wa mbali ya kum’mawa kwa kachisiyo, ndipo anapeza kuti zinali mikono 100.
-