Danieli 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo mfumuyo inalamula kuti aitane ansembe onse ochita zamatsenga,+ anthu olankhula ndi mizimu, Akasidi* ndi anthu ena ochita zamatsenga kuti adzauze mfumu maloto akewo.+ Anthu amenewa anafika ndi kuima pamaso pa mfumu.
2 Pamenepo mfumuyo inalamula kuti aitane ansembe onse ochita zamatsenga,+ anthu olankhula ndi mizimu, Akasidi* ndi anthu ena ochita zamatsenga kuti adzauze mfumu maloto akewo.+ Anthu amenewa anafika ndi kuima pamaso pa mfumu.