-
Danieli 2:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Lamulo limenelo linaperekedwa, ndipo amuna anzeru anatsala pang’ono kuphedwa, moti anthu anayamba kufunafuna Danieli ndi anzake kuti awaphe.
-