Danieli 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Popeza zilombo zikuluzikulu zimenezi zilipo zinayi,+ pali mafumu anayi amene adzauka padziko lapansi.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:17 Ulosi wa Danieli, ptsa. 130-131
17 “‘Popeza zilombo zikuluzikulu zimenezi zilipo zinayi,+ pali mafumu anayi amene adzauka padziko lapansi.+