Danieli 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu Yehova Mulungu wathu, ndinu wachifundo+ ndi wokhululuka,+ koma ife takupandukirani.+