Danieli 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno ineyo Danieli nditayang’ana, ndinangoona angelo ena awiri ataimirira.+ Mngelo wina anaimirira m’mbali mwa mtsinje tsidya lino, ndipo wina anaimirira tsidya linalo.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:5 Ulosi wa Danieli, tsa. 294
5 Ndiyeno ineyo Danieli nditayang’ana, ndinangoona angelo ena awiri ataimirira.+ Mngelo wina anaimirira m’mbali mwa mtsinje tsidya lino, ndipo wina anaimirira tsidya linalo.+