Hoseya 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Efuraimu anakhumudwitsa kwambiri Mulungu.+ Magazi amene iye anakhetsa ali pa iyeyo+ ndipo Ambuye Wamkulu adzamubwezera chitonzo chake.”+
14 Efuraimu anakhumudwitsa kwambiri Mulungu.+ Magazi amene iye anakhetsa ali pa iyeyo+ ndipo Ambuye Wamkulu adzamubwezera chitonzo chake.”+