Yoweli 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Patsogolo pawo moto wawononga+ ndipo kumbuyo kwawo moto walawilawi ukunyeketsa.+ Patsogolo pawo pali dziko ngati la Edeni+ koma kumbuyo kwawo kuli chipululu chowonongeka ndipo palibe chilichonse chopulumuka.
3 Patsogolo pawo moto wawononga+ ndipo kumbuyo kwawo moto walawilawi ukunyeketsa.+ Patsogolo pawo pali dziko ngati la Edeni+ koma kumbuyo kwawo kuli chipululu chowonongeka ndipo palibe chilichonse chopulumuka.