-
Yoweli 2:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Iwo sakankhanakankhana ndipo amayendabe ngati mwamuna wamphamvu amene akuyenda panjira yake. Wina akalasidwa ndi kugwa enawo sabwerera m’mbuyo.
-