Yoweli 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sonkhanitsani anthu onse pamodzi ndipo muyeretse mpingo.+ Sonkhanitsani amuna achikulire. Sonkhanitsani pamodzi ana ndi makanda oyamwa.+ Mkwati atuluke m’chipinda chake ndipo mkwatibwi atuluke kumalo ake ogona. Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:16 Tsiku la Yehova, tsa. 137
16 Sonkhanitsani anthu onse pamodzi ndipo muyeretse mpingo.+ Sonkhanitsani amuna achikulire. Sonkhanitsani pamodzi ana ndi makanda oyamwa.+ Mkwati atuluke m’chipinda chake ndipo mkwatibwi atuluke kumalo ake ogona.