-
Yoweli 2:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ndidzakuchotserani mdani wa kumpoto+ kuti akhale kutali ndi inu. Ndidzamuthamangitsira kudziko lopanda madzi ndi labwinja, nkhope yake itayang’ana kunyanja ya kum’mawa*+ ndipo nkhongo yake italoza kunyanja ya kumadzulo.*+ Fungo lake lonunkha lidzamveka ndipo fungo lake loipalo lidzapitirizabe kumveka+ pakuti Mulungu adzachita zinthu zazikulu.’
-