-
Zekariya 5:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako mngelo amene anali kulankhula ndi ine uja anandiyandikira n’kundiuza kuti: “Kweza maso ako uone chimene chikubwera.”
-