Zekariya 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mngelo uja anandiuza kuti: “Mkazi ameneyu dzina lake ndi Kuipa.” Kenako anamukankha n’kumubwezera m’chiwiya choyezera chokwana muyezo wa efacho,+ ndipo anavundikira chiwiyacho ndi chivundikiro chake chamtovu chija. Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:8 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2017, tsa. 24
8 Mngelo uja anandiuza kuti: “Mkazi ameneyu dzina lake ndi Kuipa.” Kenako anamukankha n’kumubwezera m’chiwiya choyezera chokwana muyezo wa efacho,+ ndipo anavundikira chiwiyacho ndi chivundikiro chake chamtovu chija.