Zekariya 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 M’chaka chachinayi cha ulamuliro wa Mfumu Dariyo,+ Yehova analankhula ndi Zekariya pa tsiku lachinayi m’mwezi wa 9, umene ndi mwezi wa Kisilevi.+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), ptsa. 2140, 2244
7 M’chaka chachinayi cha ulamuliro wa Mfumu Dariyo,+ Yehova analankhula ndi Zekariya pa tsiku lachinayi m’mwezi wa 9, umene ndi mwezi wa Kisilevi.+