Malaki 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu mukundinyoza kwambiri+ ndipo mukundibera. Mtundu wanu wonsewu ukuchita zimenezi.