Mateyu 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Musaganize kuti ndinabwera kudzawononga Chilamulo+ kapena Zolemba za aneneri. Sindinabwere kudzaziwononga koma kudzazikwaniritsa.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:17 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 86-87 Nsanja ya Olonda,2/1/2010, ptsa. 12-134/15/1987, tsa. 26
17 “Musaganize kuti ndinabwera kudzawononga Chilamulo+ kapena Zolemba za aneneri. Sindinabwere kudzaziwononga koma kudzazikwaniritsa.+