Mateyu 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kapena simunawerenge m’Chilamulo,+ kuti pa sabata ansembe m’kachisi anali kuchita zinthu mosalabadira kupatulika kwa tsiku la sabata koma anakhalabe osalakwa?+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:5 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 76-77 Nsanja ya Olonda,1/15/1987, tsa. 23
5 Kapena simunawerenge m’Chilamulo,+ kuti pa sabata ansembe m’kachisi anali kuchita zinthu mosalabadira kupatulika kwa tsiku la sabata koma anakhalabe osalakwa?+