-
Mateyu 12:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Pambuyo pake anam’bweretsera munthu wogwidwa chiwanda, amenenso anali wakhungu ndi wosalankhula, ndipo iye anam’chiritsa, moti munthuyo analankhula ndiponso anaona.
-