Mateyu 13:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 “Ufumu wakumwamba uli ngati chuma chobisika m’munda, chimene munthu anachipeza n’kuchibisa. Chifukwa cha chimwemwe chimene anali nacho, anapita kukagulitsa+ zinthu zonse zimene anali nazo n’kukagula mundawo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:44 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 110-111 Nsanja ya Olonda,12/15/2014, tsa. 104/15/1987, ptsa. 8-9 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 65-66
44 “Ufumu wakumwamba uli ngati chuma chobisika m’munda, chimene munthu anachipeza n’kuchibisa. Chifukwa cha chimwemwe chimene anali nacho, anapita kukagulitsa+ zinthu zonse zimene anali nazo n’kukagula mundawo.+
13:44 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 110-111 Nsanja ya Olonda,12/15/2014, tsa. 104/15/1987, ptsa. 8-9 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 65-66