Mateyu 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Tsopano tikupita ku Yerusalemu. Kumeneku, Mwana wa munthu akaperekedwa kwa ansembe aakulu ndi alembi, ndipo akamuweruza kuti aphedwe.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:18 Yesu—Ndi Njira, tsa. 228 Nsanja ya Olonda,9/1/1989, tsa. 8
18 “Tsopano tikupita ku Yerusalemu. Kumeneku, Mwana wa munthu akaperekedwa kwa ansembe aakulu ndi alembi, ndipo akamuweruza kuti aphedwe.+