Mateyu 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo inatuma akapolo ake kuti akaitane anthu oitanidwa ku phwando laukwati,+ koma anthuwo sanafune kubwera.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:3 Yesu—Ndi Njira, tsa. 248 Nsanja ya Olonda,1/15/2008, tsa. 311/15/1990, tsa. 8
3 Ndipo inatuma akapolo ake kuti akaitane anthu oitanidwa ku phwando laukwati,+ koma anthuwo sanafune kubwera.+