Mateyu 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atsogoleri akhungu inu,+ amene mumasefa zakumwa zanu kuti muchotsemo kanyerere+ koma mumameza ngamila.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:24 Yesu—Ndi Njira, tsa. 253 Nsanja ya Olonda,9/1/2002, tsa. 102/15/1990, tsa. 9
24 Atsogoleri akhungu inu,+ amene mumasefa zakumwa zanu kuti muchotsemo kanyerere+ koma mumameza ngamila.+