Mateyu 23:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mfarisi wakhungu+ iwe, yeretsa mkati mwa kapu+ ndi mbale choyamba, kuti kunja kwakenso kukhale koyera. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:26 Yesu—Ndi Njira, tsa. 254
26 Mfarisi wakhungu+ iwe, yeretsa mkati mwa kapu+ ndi mbale choyamba, kuti kunja kwakenso kukhale koyera.