Mateyu 24:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Chotero anthu akadzakuuzani kuti, ‘Taonani! Ali m’chipululu,’ musadzapiteko. Akadzati, ‘Taonani! Ali m’zipinda zamkati,’ musadzakhulupirire zimenezo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:26 Nsanja ya Olonda,5/1/1993, tsa. 12
26 Chotero anthu akadzakuuzani kuti, ‘Taonani! Ali m’chipululu,’ musadzapiteko. Akadzati, ‘Taonani! Ali m’zipinda zamkati,’ musadzakhulupirire zimenezo.+