Mateyu 24:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 mbuye wa kapoloyo adzabwera pa tsiku limene iye sakuyembekezera ndi pa ola+ limene sakulidziwa.