Mateyu 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Pa mapeto pake kunabwera kapolo amene analandira talente imodzi uja,+ ndipo anati, ‘Ambuye, ndinadziwa kuti inu ndinu munthu wovuta. Mumakolola kumene simunafese, ndipo mumatuta tirigu kumene simunapete.
24 “Pa mapeto pake kunabwera kapolo amene analandira talente imodzi uja,+ ndipo anati, ‘Ambuye, ndinadziwa kuti inu ndinu munthu wovuta. Mumakolola kumene simunafese, ndipo mumatuta tirigu kumene simunapete.