Maliko 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Yohane ataponyedwa m’ndende, Yesu anapita ku Galileya+ kukalalikira uthenga wabwino wa Mulungu+
14 Tsopano Yohane ataponyedwa m’ndende, Yesu anapita ku Galileya+ kukalalikira uthenga wabwino wa Mulungu+