Maliko 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 kuti: “Nthawi yoikidwiratu yakwaniritsidwa!+ Ufumu wa Mulungu wayandikira! Lapani+ anthu inu! Khulupirirani uthenga wabwino!” Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:15 Kufotokoza Mavesi a m’Baibulo, article 1 Nsanja ya Olonda,2/15/2008, tsa. 281/15/2003, tsa. 10
15 kuti: “Nthawi yoikidwiratu yakwaniritsidwa!+ Ufumu wa Mulungu wayandikira! Lapani+ anthu inu! Khulupirirani uthenga wabwino!”