Maliko 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kachiwirinso Yesu analowa m’sunagoge. Mmenemo munali munthu wa dzanja lopuwala.+