-
Maliko 6:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Nthawi yomweyo anapita kwa mfumuyo mofulumira, ndi kupempha kuti: “Ndikufuna mundipatse mutu wa Yohane M’batizi m’mbale pompano.”
-