Maliko 6:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Iye anawauza kuti: “Inuyo bwerani kuno, tipite kwatokha kopanda anthu+ kuti mupumule pang’ono.”+ Pakuti ambiri anali kubwera ndi kupita, ndipo analibe nthawi yopuma, ngakhale yoti adye chakudya.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:31 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 17 Nsanja ya Olonda,2/15/2000, tsa. 21
31 Iye anawauza kuti: “Inuyo bwerani kuno, tipite kwatokha kopanda anthu+ kuti mupumule pang’ono.”+ Pakuti ambiri anali kubwera ndi kupita, ndipo analibe nthawi yopuma, ngakhale yoti adye chakudya.+