Maliko 10:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Choncho, Yesu anaima ndi kunena kuti: “Muitaneni.” Iwo anaitana wakhunguyo, ndi kumuuza kuti: “Limba mtima, nyamuka, akukuitana.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:49 Yesu—Ndi Njira, tsa. 230 Nsanja ya Olonda,9/15/1989, tsa. 8
49 Choncho, Yesu anaima ndi kunena kuti: “Muitaneni.” Iwo anaitana wakhunguyo, ndi kumuuza kuti: “Limba mtima, nyamuka, akukuitana.”+