Maliko 13:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chimodzimodzi inunso, mukadzaona zinthu izi zikuchitika, dziwani kuti iye ali pafupi. Dziwani kuti ali pakhomo penipeni.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:29 Yesu—Ndi Njira, tsa. 258 Nsanja ya Olonda,4/1/1990, tsa. 25
29 Chimodzimodzi inunso, mukadzaona zinthu izi zikuchitika, dziwani kuti iye ali pafupi. Dziwani kuti ali pakhomo penipeni.+