Maliko 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma Yesu anati: “Mulekeni. N’chifukwa chiyani mukum’vutitsa mayiyu? Iyetu wandichitira zinthu zabwino.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:6 Nsanja ya Olonda,4/15/1999, tsa. 16
6 Koma Yesu anati: “Mulekeni. N’chifukwa chiyani mukum’vutitsa mayiyu? Iyetu wandichitira zinthu zabwino.+