Maliko 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo chisoni chinawagwira ndipo anayamba kumufunsa mmodzimmodzi kuti: “Kodi ndine kapena?”+