Maliko 14:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndiyeno anawauza kuti: “Moyo wanga ukumva chisoni chofa nacho.+ Khalani pompano ndipo mukhalebe maso.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:34 Yesu—Ndi Njira, tsa. 282 Nsanja ya Olonda,10/1/1990, tsa. 8
34 Ndiyeno anawauza kuti: “Moyo wanga ukumva chisoni chofa nacho.+ Khalani pompano ndipo mukhalebe maso.”+