Maliko 14:66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Tsopano pamene Petulo anali m’munsi, m’bwalo lamkati, mmodzi wa atsikana antchito a mkulu wa ansembe anabwera.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:66 Yesu—Ndi Njira, tsa. 288 Nsanja ya Olonda,11/15/1990, tsa. 8
66 Tsopano pamene Petulo anali m’munsi, m’bwalo lamkati, mmodzi wa atsikana antchito a mkulu wa ansembe anabwera.+