Maliko 14:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Ataona Petulo akuwotha moto, anamuyang’anitsitsa ndi kunena kuti: “Inunso munali ndi Yesu, Mnazareti uja.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:67 Yesu—Ndi Njira, tsa. 288 Nsanja ya Olonda,11/15/1990, tsa. 8
67 Ataona Petulo akuwotha moto, anamuyang’anitsitsa ndi kunena kuti: “Inunso munali ndi Yesu, Mnazareti uja.”+