Luka 2:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Choncho pamene anali ndi zaka 12, iwo anapita naye kumeneko malinga ndi mwambo+ wa chikondwererocho, Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:42 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 10 1. Kuwala Kwenikweni kwa Dziko Malifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu Zimene Yesu anachita kukachisi ali ndi zaka 12 (gnj 1 1:04:00–1:09:40)
42 Choncho pamene anali ndi zaka 12, iwo anapita naye kumeneko malinga ndi mwambo+ wa chikondwererocho,