Luka 6:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Nanga n’chifukwa chiyani umayang’ana kachitsotso kamene kali m’diso la m’bale wako, koma osaona mtanda wa denga la nyumba umene uli m’diso lako?+
41 Nanga n’chifukwa chiyani umayang’ana kachitsotso kamene kali m’diso la m’bale wako, koma osaona mtanda wa denga la nyumba umene uli m’diso lako?+