Luka 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Analinso ndi amayi+ ena amene anawatulutsa mizimu yoipa ndi kuwachiritsa matenda awo. Ena mwa iwo anali Mariya wotchedwanso Mmagadala, amene anamutulutsa ziwanda 7.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:2 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo, Nsanja ya Olonda,6/1/2003, ptsa. 4-5
2 Analinso ndi amayi+ ena amene anawatulutsa mizimu yoipa ndi kuwachiritsa matenda awo. Ena mwa iwo anali Mariya wotchedwanso Mmagadala, amene anamutulutsa ziwanda 7.+