Luka 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zimene zinagwera paminga, ndi anthu amene amva mawu a Mulungu. Koma chifukwa chotengeka ndi nkhawa, chuma ndi zosangalatsa za moyo uno,+ amalephera kukula bwino, ndipo zipatso zawo sizikhwima.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:14 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2020, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,2/1/2003, ptsa. 12-1311/1/1999, tsa. 16
14 Zimene zinagwera paminga, ndi anthu amene amva mawu a Mulungu. Koma chifukwa chotengeka ndi nkhawa, chuma ndi zosangalatsa za moyo uno,+ amalephera kukula bwino, ndipo zipatso zawo sizikhwima.+
8:14 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2020, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,2/1/2003, ptsa. 12-1311/1/1999, tsa. 16