Luka 9:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndiyeno Yohane ananena kuti: “Mlangizi, tinaona munthu wina akutulutsa ziwanda+ m’dzina lanu, choncho ife tinamuletsa+ chifukwa sakukutsatirani pamodzi ndi ife.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:49 Yesu—Ndi Njira, tsa. 150 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, tsa. 8
49 Ndiyeno Yohane ananena kuti: “Mlangizi, tinaona munthu wina akutulutsa ziwanda+ m’dzina lanu, choncho ife tinamuletsa+ chifukwa sakukutsatirani pamodzi ndi ife.”+