Luka 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Tsopano pamene anali kuyenda, analowa m’mudzi wina. Kumeneko mayi wina dzina lake Marita+ anamulandira m’nyumba mwake monga mlendo. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:38 Yesu—Ndi Njira, tsa. 174 Nsanja ya Olonda,8/1/1988, tsa. 8
38 Tsopano pamene anali kuyenda, analowa m’mudzi wina. Kumeneko mayi wina dzina lake Marita+ anamulandira m’nyumba mwake monga mlendo.