Luka 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akapita nanu kumabwalo amilandu, ndi kwa akuluakulu aboma, komanso kwa olamulira, musade nkhawa kuti mukadziteteza bwanji kapena mukanena chiyani.+
11 Akapita nanu kumabwalo amilandu, ndi kwa akuluakulu aboma, komanso kwa olamulira, musade nkhawa kuti mukadziteteza bwanji kapena mukanena chiyani.+