Luka 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo ndidzauza+ moyo wanga kuti: “Moyo wangawe, uli ndi zinthu zambiri zabwino mwakuti zisungika kwa zaka zambiri. Ungoti phee tsopano, ndipo udye, umwe ndi kusangalala.”’+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:19 Nsanja ya Olonda,8/1/2007, ptsa. 27-28
19 Ndipo ndidzauza+ moyo wanga kuti: “Moyo wangawe, uli ndi zinthu zambiri zabwino mwakuti zisungika kwa zaka zambiri. Ungoti phee tsopano, ndipo udye, umwe ndi kusangalala.”’+