Luka 12:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Inuyo mukhale ngati anthu amene akuyembekezera kubwera kwa mbuye wawo+ kuchokera ku ukwati,+ kuti akafika ndi kugogoda+ amutsegulire mwamsanga.
36 Inuyo mukhale ngati anthu amene akuyembekezera kubwera kwa mbuye wawo+ kuchokera ku ukwati,+ kuti akafika ndi kugogoda+ amutsegulire mwamsanga.