Luka 12:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Odala ndi akapolo amene mbuye wawo pofika adzawapeza akudikira!+ Ndithu ndikukuuzani, Iye adzamanga m’chiuno+ mwake ndi kuwakhazika patebulo kuti adye chakudya ndipo adzawatumikira.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:37 Nsanja ya Olonda,10/1/1988, tsa. 9
37 Odala ndi akapolo amene mbuye wawo pofika adzawapeza akudikira!+ Ndithu ndikukuuzani, Iye adzamanga m’chiuno+ mwake ndi kuwakhazika patebulo kuti adye chakudya ndipo adzawatumikira.+