Luka 12:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma dziwani kuti mwininyumba atadziwa nthawi yobwera mbala, angakhale maso ndipo sangalole kuti mbala zithyole ndi kulowa m’nyumba mwake.+
39 Koma dziwani kuti mwininyumba atadziwa nthawi yobwera mbala, angakhale maso ndipo sangalole kuti mbala zithyole ndi kulowa m’nyumba mwake.+