Luka 12:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Kenako anauzanso khamu la anthulo kuti: “Mukaona mtambo ukukwera chakumadzulo, nthawi yomweyo mumanena kuti, ‘Kukubwera chimvula,’ ndipo chimabweradi.+
54 Kenako anauzanso khamu la anthulo kuti: “Mukaona mtambo ukukwera chakumadzulo, nthawi yomweyo mumanena kuti, ‘Kukubwera chimvula,’ ndipo chimabweradi.+